Ekisodo 28:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 “Koma iwe patula Aroni m’bale wako pamodzi ndi ana ake pakati pa ana a Isiraeli, ndipo Aroniyo+ atumikire monga wansembe wanga pamodzi ndi ana akewo,+ Nadabu, Abihu,+ Eleazara ndi Itamara.+ Deuteronomo 33:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndipo kwa Levi anati:+“Tumimu ndi Urimu+ wanu ndizo za munthu wokhulupirika kwa inu,+Amene munamuyesa pa Masa.+Munayamba kulimbana naye pafupi ndi madzi a Meriba.+
28 “Koma iwe patula Aroni m’bale wako pamodzi ndi ana ake pakati pa ana a Isiraeli, ndipo Aroniyo+ atumikire monga wansembe wanga pamodzi ndi ana akewo,+ Nadabu, Abihu,+ Eleazara ndi Itamara.+
8 Ndipo kwa Levi anati:+“Tumimu ndi Urimu+ wanu ndizo za munthu wokhulupirika kwa inu,+Amene munamuyesa pa Masa.+Munayamba kulimbana naye pafupi ndi madzi a Meriba.+