1 Mbiri 29:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kenako Davide anauza mpingo wonse kuti:+ “Tsopano tamandani+ Yehova Mulungu wanu!” Choncho mpingo wonse unayamba kutamanda Yehova Mulungu wa makolo awo, ndipo anagwada+ n’kuwerama mpaka nkhope zawo pansi+ kwa Yehova ndi kwa mfumu. Salimo 68:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Anthu inu, imbirani Mulungu, muimbireni nyimbo zotamanda dzina lake.+Muimbireni nyimbo Iye amene akudutsa m’chipululu,+Amene dzina lake ndi Ya,*+ ndipo kondwerani pamaso pake.
20 Kenako Davide anauza mpingo wonse kuti:+ “Tsopano tamandani+ Yehova Mulungu wanu!” Choncho mpingo wonse unayamba kutamanda Yehova Mulungu wa makolo awo, ndipo anagwada+ n’kuwerama mpaka nkhope zawo pansi+ kwa Yehova ndi kwa mfumu.
4 Anthu inu, imbirani Mulungu, muimbireni nyimbo zotamanda dzina lake.+Muimbireni nyimbo Iye amene akudutsa m’chipululu,+Amene dzina lake ndi Ya,*+ ndipo kondwerani pamaso pake.