Salimo 25:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 M’njira zonse za Yehova muli kukoma mtima kosatha ndi choonadiKwa anthu osunga pangano+ lake ndi zikumbutso zake.+ Salimo 71:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Inenso ndidzakutamandani ndi chipangizo cha zingwe,+Ndidzatamanda choonadi chanu, inu Mulungu.+Ndidzaimba nyimbo zokutamandani ndi zeze, Inu Woyera wa Isiraeli.+ Salimo 91:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Adzakutchinjiriza ndi mapiko ake,+Udzathawira pansi pa mapiko ake.+Choonadi chake+ chidzakhala chishango chako+ chachikulu ndi malo ako achitetezo. Yesaya 10:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 M’tsiku limenelo, otsala a Isiraeli+ ndi opulumuka a nyumba ya Yakobo sadzadaliranso yemwe akuwamenya,+ koma ndi mtima wonse adzadalira Yehova, Woyera wa Isiraeli.+ Luka 1:55 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 monga momwe anauzira makolo athu akale, Abulahamu ndi mbewu yake.”+
10 M’njira zonse za Yehova muli kukoma mtima kosatha ndi choonadiKwa anthu osunga pangano+ lake ndi zikumbutso zake.+
22 Inenso ndidzakutamandani ndi chipangizo cha zingwe,+Ndidzatamanda choonadi chanu, inu Mulungu.+Ndidzaimba nyimbo zokutamandani ndi zeze, Inu Woyera wa Isiraeli.+
4 Adzakutchinjiriza ndi mapiko ake,+Udzathawira pansi pa mapiko ake.+Choonadi chake+ chidzakhala chishango chako+ chachikulu ndi malo ako achitetezo.
20 M’tsiku limenelo, otsala a Isiraeli+ ndi opulumuka a nyumba ya Yakobo sadzadaliranso yemwe akuwamenya,+ koma ndi mtima wonse adzadalira Yehova, Woyera wa Isiraeli.+