Deuteronomo 5:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Muyende m’njira yonse imene Yehova Mulungu wanu wakulamulani,+ kuti mukhale ndi moyo ndi kuti zinthu zikuyendereni bwino+ ndiponso kuti mutalikitsedi masiku anu m’dziko limene mudzalitenga kukhala lanu. Yeremiya 7:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma ndinawalamula kuti: “Muzimvera mawu anga,+ ndipo ndidzakhala Mulungu wanu,+ inuyo mudzakhala anthu anga. Muziyenda m’njira+ imene ndidzakulamulani, kuti zinthu zikuyendereni bwino.”’+ Yohane 14:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Amene ali ndi malamulo anga ndipo amawasunga, ameneyo ndiye amene amandikonda.+ Komanso wondikonda ine, Atate wanga adzamukondanso. Inenso ndidzamukonda ndipo ndidzadzionetsera bwinobwino kwa iye.”
33 Muyende m’njira yonse imene Yehova Mulungu wanu wakulamulani,+ kuti mukhale ndi moyo ndi kuti zinthu zikuyendereni bwino+ ndiponso kuti mutalikitsedi masiku anu m’dziko limene mudzalitenga kukhala lanu.
23 Koma ndinawalamula kuti: “Muzimvera mawu anga,+ ndipo ndidzakhala Mulungu wanu,+ inuyo mudzakhala anthu anga. Muziyenda m’njira+ imene ndidzakulamulani, kuti zinthu zikuyendereni bwino.”’+
21 Amene ali ndi malamulo anga ndipo amawasunga, ameneyo ndiye amene amandikonda.+ Komanso wondikonda ine, Atate wanga adzamukondanso. Inenso ndidzamukonda ndipo ndidzadzionetsera bwinobwino kwa iye.”