Yakobo 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Aliyense wosunga Chilamulo akalakwitsa mbali imodzi, walakwira malamulo onse.+ 1 Yohane 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chifukwa kukonda+ Mulungu kumatanthauza kusunga malamulo ake, ndipo malamulo akewo+ ndi osalemetsa.+
3 Chifukwa kukonda+ Mulungu kumatanthauza kusunga malamulo ake, ndipo malamulo akewo+ ndi osalemetsa.+