Salimo 19:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Malamulo+ ochokera kwa Yehova ndi olungama,+ amasangalatsa mtima.+Chilamulo+ cha Yehova ndi choyera,+ chimatsegula maso.+ Salimo 119:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndidzasinkhasinkha malamulo anu,+Ndipo ndidzalabadira njira zanu.+
8 Malamulo+ ochokera kwa Yehova ndi olungama,+ amasangalatsa mtima.+Chilamulo+ cha Yehova ndi choyera,+ chimatsegula maso.+