Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 16:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Ndiyeno Mose analankhula ndi Kora ndiponso khamu lonselo, kuti: “Mawa m’mawa, Yehova aonetsa amene ali wake+ ndiponso amene ali woyera.+ Aonetsa amene ayenera kuima pamaso pake,+ ndipo amene ati am’sankheyo+ adzaima pamaso pake.

  • Deuteronomo 1:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 ‘Palibe munthu ndi mmodzi yemwe mwa anthu a m’badwo woipa uwu amene adzaona dziko labwino limene ndinalumbira kuti ndidzalipereka kwa makolo anu,+

  • Deuteronomo 4:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 “Inu munaona ndi maso anu zimene Yehova anachita pa nkhani ya Baala wa ku Peori, kuti munthu aliyense amene anatsatira Baala wa ku Peori,+ Yehova Mulungu wanu anamuwononga ndi kum’chotsa pakati panu.+

  • Salimo 36:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Inu Mulungu, chilungamo chanu chili ngati mapiri anu.+

      Chiweruzo chanu ndi chozama kwambiri ngati madzi akuya.+

      Inu Yehova, mumapulumutsa munthu ndiponso nyama.+

  • Salimo 105:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Kumbukirani ntchito zodabwitsa zimene wachita,+

      Kumbukirani zozizwitsa zake ndi zigamulo zotuluka m’kamwa mwake,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena