Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 3:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Atatero maso awo anatseguka, ndipo anazindikira kuti ali maliseche.+ Choncho anadzisokera masamba a mkuyu n’kupanga zovala zomangira m’chiuno.+

  • Salimo 25:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Inu Mulungu wanga, chikhulupiriro changa chili mwa inu.+

      Musalole kuti ndichite manyazi.

      Adani anga asakondwere chifukwa cha masautso anga.+

  • Salimo 119:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Pamenepo sindikanachita manyazi,+

      Pamene ndikulabadira malamulo anu onse.+

  • 1 Yohane 2:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Tsopano inu ana anga okondedwa,+ khalanibe ogwirizana+ naye, kuti akadzaonetsedwa,+ tidzakhale ndi ufulu wa kulankhula.+ Kutinso tisadzachititsidwe manyazi ndi kuchotsedwa kwa iye pa nthawi ya kukhalapo*+ kwake.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena