Salimo 19:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chilamulo+ cha Yehova ndi changwiro,+ chimabwezeretsa moyo.+Zikumbutso+ za Yehova ndi zodalirika,+ zimapatsa nzeru munthu wosadziwa zinthu.+ Salimo 119:79 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 79 Anthu okuopani abwerere kwa ine,+Chimodzimodzinso odziwa zikumbutso zanu.+
7 Chilamulo+ cha Yehova ndi changwiro,+ chimabwezeretsa moyo.+Zikumbutso+ za Yehova ndi zodalirika,+ zimapatsa nzeru munthu wosadziwa zinthu.+