Salimo 19:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 N’zolakalakika kuposa golide, kuposa golide wambiri woyengeka bwino.+N’zotsekemera* kuposa uchi,+ inde kuposa uchi umene ukukha m’zisa.+ Miyambo 8:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakuti nzeru n’zamtengo wapatali kuposa miyala ya korali,+ ndipo zosangalatsa zonse sizingafanane nazo.+ Miyambo 24:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mwana wanga, idya uchi chifukwa ndi wabwino, ndipo uchi wotsekemera wochokera pazisa za njuchi uuike m’kamwa mwako.+
10 N’zolakalakika kuposa golide, kuposa golide wambiri woyengeka bwino.+N’zotsekemera* kuposa uchi,+ inde kuposa uchi umene ukukha m’zisa.+
11 Pakuti nzeru n’zamtengo wapatali kuposa miyala ya korali,+ ndipo zosangalatsa zonse sizingafanane nazo.+
13 Mwana wanga, idya uchi chifukwa ndi wabwino, ndipo uchi wotsekemera wochokera pazisa za njuchi uuike m’kamwa mwako.+