Salimo 93:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Zikumbutso zanu ndi zodalirika zedi.+Chiyero ndi choyenera nyumba yanu+ mpaka muyaya, inu Yehova.+