Salimo 48:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Gubani mozungulira Ziyoni, anthu inu, ndipo yendayendani mmenemo,+Werengani nsanja zake.+