Salimo 66:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mwachititsa munthu wamba kutipondaponda.+Tadutsa pamoto ndi pamadzi,+Ndipo inu mwatipatsa mpumulo.+ Salimo 141:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mafupa athu amwazika pakamwa pa Manda,Mofanana ndi zidutswa zimene zimamwazika pansi pamene munthu akuwaza ndi kung’amba mtengo.+ Yesaya 51:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndidzachiika m’manja mwa amene akukuvutitsa,+ amene akukuuza kuti, ‘Werama kuti tiwolokere pamsana pako,’ amene akuona msana wako ngati pansi popondapo, ndiponso ngati njira yowolokerapo.”+
12 Mwachititsa munthu wamba kutipondaponda.+Tadutsa pamoto ndi pamadzi,+Ndipo inu mwatipatsa mpumulo.+
7 Mafupa athu amwazika pakamwa pa Manda,Mofanana ndi zidutswa zimene zimamwazika pansi pamene munthu akuwaza ndi kung’amba mtengo.+
23 Ndidzachiika m’manja mwa amene akukuvutitsa,+ amene akukuuza kuti, ‘Werama kuti tiwolokere pamsana pako,’ amene akuona msana wako ngati pansi popondapo, ndiponso ngati njira yowolokerapo.”+