Salimo 83:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iwo anena kuti: “Bwerani tiwafafanize kuti asakhalenso mtundu,+Ndi kuti dzina la Isiraeli lisakumbukikenso.”+ Salimo 137:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Inu Yehova, kumbukirani+ zimene ana a Edomu+ ananena pa tsiku limene Yerusalemu anawonongedwa,+Iwo anati: “Fafanizani mzindawo! Ufafanizeni mpaka pamaziko ake!”+
4 Iwo anena kuti: “Bwerani tiwafafanize kuti asakhalenso mtundu,+Ndi kuti dzina la Isiraeli lisakumbukikenso.”+
7 Inu Yehova, kumbukirani+ zimene ana a Edomu+ ananena pa tsiku limene Yerusalemu anawonongedwa,+Iwo anati: “Fafanizani mzindawo! Ufafanizeni mpaka pamaziko ake!”+