Salimo 118:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Wodala ndi Iye wobwera m’dzina la Yehova.+Takudalitsani anthu inu potuluka m’nyumba ya Yehova.+