Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 30:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Zimenezi zinam’vutitsa maganizo kwambiri Davide+ chifukwanso anthu anali kukambirana zom’ponya miyala.+ Anthuwo anali kukambirana zimenezi chifukwa aliyense wa iwo anali wokwiya kwambiri+ poona zimene zachitikira ana awo aamuna ndi ana awo aakazi. Choncho, Davide anadzilimbitsa mwa Yehova Mulungu wake.+

  • Salimo 42:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 N’chifukwa chiyani ukutaya mtima, moyo wangawe?+

      Ndipo n’chifukwa chiyani ukusautsika mkati mwanga?+

      Yembekezera Mulungu,+

      Ndipo ndidzamutamanda pakuti iye ndiye mpulumutsi wanga wamkulu.+

  • Salimo 62:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 62 Ndithudi, moyo wanga ukuyembekezera Mulungu modekha.+

      Chipulumutso changa chidzachokera kwa iye.+

  • Yesaya 30:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Pakuti Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, Woyera wa Isiraeli,+ wanena kuti: “Anthu inu mukabwerera kwa ine n’kusiya zimene mukuchita, mudzapulumuka. Mudzakhala amphamvu mukakhala osatekeseka ndi achikhulupiriro.”+ Koma inu simunafune.+

  • Maliro 3:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Ndi bwino kuti munthu ayembekezere+ chipulumutso cha Yehova+ moleza mtima.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena