Mateyu 18:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 ndi kunena kuti: “Ndithu ndikukuuzani, Mukapanda kutembenuka n’kukhala ngati ana aang’ono,+ simudzalowa mu ufumu wakumwamba.+ 1 Akorinto 14:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Abale, musakhale ana aang’ono pa luntha la kuzindikira,+ koma khalani tiana pa zoipa,+ ndipo pa luntha la kuzindikira khalani aakulu msinkhu.+
3 ndi kunena kuti: “Ndithu ndikukuuzani, Mukapanda kutembenuka n’kukhala ngati ana aang’ono,+ simudzalowa mu ufumu wakumwamba.+
20 Abale, musakhale ana aang’ono pa luntha la kuzindikira,+ koma khalani tiana pa zoipa,+ ndipo pa luntha la kuzindikira khalani aakulu msinkhu.+