Salimo 115:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iwe Isiraeli, khulupirira Yehova.+Iye ndiye thandizo lako ndi chishango chako.+ Salimo 130:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Isiraeli ayembekezere Yehova,+Pakuti Yehova amasonyeza kukoma mtima kosatha.+Iye ali ndi mphamvu zochuluka zowombolera anthu ake.+ Yeremiya 17:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Wodala ndi munthu aliyense amene amakhulupirira Yehova, amene amadalira Yehova.+ Mika 7:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma ine ndidzadikirira Yehova.+ Ndidzayembekezera moleza mtima Mulungu wa chipulumutso changa.+ Mulungu wanga adzandimvera.+
7 Isiraeli ayembekezere Yehova,+Pakuti Yehova amasonyeza kukoma mtima kosatha.+Iye ali ndi mphamvu zochuluka zowombolera anthu ake.+
7 Koma ine ndidzadikirira Yehova.+ Ndidzayembekezera moleza mtima Mulungu wa chipulumutso changa.+ Mulungu wanga adzandimvera.+