Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 29:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Kenako utenge mafuta odzozera+ ndi kuwathira pamutu pake ndi kum’dzoza.+

  • Ekisodo 30:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Zinthu zimenezi upangire mafuta ogwiritsa ntchito pa kudzoza kopatulika, mafuta onunkhira osakaniza mwaluso.+ Akhale mafuta ogwiritsa ntchito pa kudzoza kopatulika.+

  • Levitiko 21:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 “‘Ndipo mkulu wa ansembe wokhala pakati pa abale ake ansembe, wodzozedwa mafuta pamutu pake,+ ndi kupatsidwa mphamvu* kuti avale zovala zaunsembe,+ asalekerere tsitsi lake osalisamala+ ndipo asang’ambe zovala zake.+

  • Salimo 141:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Wolungama akandimenya ndiye kuti wandisonyeza kukoma mtima kosatha,+

      Ndipo akandidzudzula ndiye kuti wandidzoza mafuta pamutu panga,+

      Mafuta amene mutu wanga sungawakane.+

      Pakuti ndidzapemphererabe anthu olungama ngakhale pamene masoka awagwera.+

  • Miyambo 27:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Mafuta ndi zofukiza zonunkhira+ n’zimene zimasangalatsa mtima, chimodzimodzinso kukoma kwa mnzako chifukwa cha malangizo ake ochokera pansi pa mtima, kumasangalatsa mtima.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena