Salimo 106:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 106 Tamandani Ya, anthu inu!+Yamikani Yehova, chifukwa iye ndi wabwino.+Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+ Salimo 119:68 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 68 Inu ndinu wabwino ndipo mukuchita zabwino.+Ndiphunzitseni malamulo anu.+ Mateyu 19:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Iye anamuyankha kuti: “N’chifukwa chiyani ukundifunsa chimene chili chabwino? Pali Mmodzi yekha amene ali wabwino.+ Chotero ngati ukufuna kukapeza moyo, uzisunga malamulo nthawi zonse.”+
106 Tamandani Ya, anthu inu!+Yamikani Yehova, chifukwa iye ndi wabwino.+Pakuti kukoma mtima kwake kosatha kudzakhalapobe mpaka kalekale.+
17 Iye anamuyankha kuti: “N’chifukwa chiyani ukundifunsa chimene chili chabwino? Pali Mmodzi yekha amene ali wabwino.+ Chotero ngati ukufuna kukapeza moyo, uzisunga malamulo nthawi zonse.”+