Salimo 33:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yamikani Yehova poimba zeze.+Muimbireni nyimbo zomutamanda ndi choimbira cha zingwe 10.+ Yesaya 24:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Nyimbo zachisangalalo zoimbidwa ndi maseche zasiya kumveka. Phokoso la anthu okondwa kwambiri silikumvekanso. Nyimbo zachisangalalo zoimbidwa ndi zeze zaleka kumveka.+
8 Nyimbo zachisangalalo zoimbidwa ndi maseche zasiya kumveka. Phokoso la anthu okondwa kwambiri silikumvekanso. Nyimbo zachisangalalo zoimbidwa ndi zeze zaleka kumveka.+