Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 82:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 82 Mulungu waima pakati pa msonkhano wake,+

      Ndipo akuweruza pakati pa milungu kuti:+

  • Salimo 119:46
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  46 Komanso ndidzanena za zikumbutso zanu pamaso pa mafumu,+

      Ndipo sindidzachita manyazi.+

  • Yohane 10:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Yesu anawafunsa kuti: “Kodi m’Chilamulo chanu sanalembemo+ kuti, ‘Ine ndinati: “Inu ndinu milungu”’?+

  • 1 Akorinto 8:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Pakuti ngakhale ilipo yotchedwa “milungu,”+ kaya kumwamba+ kapena padziko lapansi,+ ndipo n’zoona ilipodi “milungu” yambiri ndi “ambuye” ambiri,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena