Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 31:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Koma ine chikhulupiriro changa chili mwa inu Yehova.+

      Ndipo ndikunena kuti: “Inu ndinu Mulungu wanga.”+

  • Salimo 91:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Ndidzauza Yehova kuti: “Inu ndinu pothawirapo panga ndi malo anga achitetezo,+

      Mulungu wanga amene ndimamukhulupirira.”+

  • Yohane 20:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Yesu anati: “Usandikangamire. Pakuti sindinakwerebe kwa Atate. Koma pita kwa abale anga+ ukawauze kuti, ‘Ine ndikukwera kwa Atate+ wanga ndi Atate wanu, kwa Mulungu wanga+ ndi Mulungu wanu.’”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena