Salimo 27:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Inu Yehova, imvani mawu anga pamene ndikuitana.+Ndikomereni mtima ndi kundiyankha.+ Salimo 28:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Imvani mawu anga ochonderera pamene ndikufuulira inu kuti mundithandize,Pamene ndikukweza manja anga,+ nditayang’ana kumene kuli chipinda chamkati cha m’malo anu opatulika.+ Salimo 55:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 Inu Mulungu, mvetserani pemphero langa.+Musanyalanyaze pempho langa lakuti mundikomere mtima.+
2 Imvani mawu anga ochonderera pamene ndikufuulira inu kuti mundithandize,Pamene ndikukweza manja anga,+ nditayang’ana kumene kuli chipinda chamkati cha m’malo anu opatulika.+