Deuteronomo 33:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Mulungu wakale lomwe ndiwo malo ako obisalamo,+Ndipo iwe uli m’manja amene adzakhalapo mpaka kalekale.+Adzapitikitsa mdani pamaso pako,+Ndipo adzanena kuti, ‘Awononge!’+ Salimo 27:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Yehova ndiye kuwala+ kwanga ndi chipulumutso changa.+Ndingaopenso ndani?+Yehova ndiye malo a chitetezo cha moyo wanga.+Ndingachitenso mantha ndi ndani?+ Salimo 28:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova ndiye mphamvu kwa anthu ake,+Iye ndi malo achitetezo odzetsa chipulumutso chachikulu kwa wodzozedwa wake.+
27 Mulungu wakale lomwe ndiwo malo ako obisalamo,+Ndipo iwe uli m’manja amene adzakhalapo mpaka kalekale.+Adzapitikitsa mdani pamaso pako,+Ndipo adzanena kuti, ‘Awononge!’+
27 Yehova ndiye kuwala+ kwanga ndi chipulumutso changa.+Ndingaopenso ndani?+Yehova ndiye malo a chitetezo cha moyo wanga.+Ndingachitenso mantha ndi ndani?+
8 Yehova ndiye mphamvu kwa anthu ake,+Iye ndi malo achitetezo odzetsa chipulumutso chachikulu kwa wodzozedwa wake.+