1 Samueli 17:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Ndiyeno Davide anawonjezera kuti: “Yehova amene anandilanditsa m’kamwa mwa mkango ndi m’kamwa mwa chimbalangondo andilanditsanso m’manja mwa Mfilisiti ameneyu.”+ Pamenepo Sauli anauza Davide kuti: “Pita, ndipo Yehova akhale nawe.”+ Salimo 144:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndidzaimbira inu amene mumapulumutsa mafumu,+Amene mumalanditsa ine Davide mtumiki wanu ku lupanga lovulaza.+
37 Ndiyeno Davide anawonjezera kuti: “Yehova amene anandilanditsa m’kamwa mwa mkango ndi m’kamwa mwa chimbalangondo andilanditsanso m’manja mwa Mfilisiti ameneyu.”+ Pamenepo Sauli anauza Davide kuti: “Pita, ndipo Yehova akhale nawe.”+
10 Ndidzaimbira inu amene mumapulumutsa mafumu,+Amene mumalanditsa ine Davide mtumiki wanu ku lupanga lovulaza.+