2 Samueli 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Choncho Davide anatumiza mithenga kwa amuna a ku Yabesi-giliyadi+ kuti akawauze kuti: “Yehova akudalitseni,+ chifukwa munasonyeza kukoma mtima kosatha+ kwa mbuye wanu Sauli mwa kumuika m’manda.+ 2 Samueli 23:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mawu omaliza amene Davide ananena ndi awa:+“Mawu a Davide mwana wa Jese,+Mawu a munthu wamphamvu amene anakwezedwa pamwamba,+Wodzozedwa+ wa Mulungu wa Yakobo,Munthu wosangalatsa wotchulidwa m’nyimbo zokoma+ za Isiraeli. Luka 4:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Pamenepo onse anayamba kumutamanda ndi kudabwa ndi mawu ogwira mtima+ otuluka pakamwa pake, mwakuti anali kunena kuti: “Kodi iyeyu si mwana wa Yosefe?”+
5 Choncho Davide anatumiza mithenga kwa amuna a ku Yabesi-giliyadi+ kuti akawauze kuti: “Yehova akudalitseni,+ chifukwa munasonyeza kukoma mtima kosatha+ kwa mbuye wanu Sauli mwa kumuika m’manda.+
23 Mawu omaliza amene Davide ananena ndi awa:+“Mawu a Davide mwana wa Jese,+Mawu a munthu wamphamvu amene anakwezedwa pamwamba,+Wodzozedwa+ wa Mulungu wa Yakobo,Munthu wosangalatsa wotchulidwa m’nyimbo zokoma+ za Isiraeli.
22 Pamenepo onse anayamba kumutamanda ndi kudabwa ndi mawu ogwira mtima+ otuluka pakamwa pake, mwakuti anali kunena kuti: “Kodi iyeyu si mwana wa Yosefe?”+