Yoswa 4:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kenako anauza ana a Isiraeli kuti: “Ana anu akamadzafunsa abambo awo m’tsogolomu kuti, ‘Kodi miyalayi ndi ya chiyani?’+ Salimo 71:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ngakhale nditakalamba ndi kumera imvi, inu Mulungu musandisiye,+Kufikira nditanena za dzanja lanu lamphamvu ku m’badwo wotsatira,+Kufikira nditanena za mphamvu zanu kwa onse obwera m’tsogolo.+ Yesaya 38:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Munthu wamoyo, amene akupuma, ndi amene angakutamandeni,+Ngati mmene ineyo ndikuchitira lero.+Bambo akhoza kuphunzitsa+ ana ake za kukhulupirika kwanu.
21 Kenako anauza ana a Isiraeli kuti: “Ana anu akamadzafunsa abambo awo m’tsogolomu kuti, ‘Kodi miyalayi ndi ya chiyani?’+
18 Ngakhale nditakalamba ndi kumera imvi, inu Mulungu musandisiye,+Kufikira nditanena za dzanja lanu lamphamvu ku m’badwo wotsatira,+Kufikira nditanena za mphamvu zanu kwa onse obwera m’tsogolo.+
19 Munthu wamoyo, amene akupuma, ndi amene angakutamandeni,+Ngati mmene ineyo ndikuchitira lero.+Bambo akhoza kuphunzitsa+ ana ake za kukhulupirika kwanu.