Salimo 19:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Zakumwamba zikulengeza ulemerero wa Mulungu.+Ndipo m’mlengalenga mukufotokoza ntchito ya manja ake.+ Salimo 103:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Tamandani Yehova inu ntchito zake zonse,+M’malo onse amene iye akulamulira.+Tamanda Yehova, iwe moyo wanga.+ Salimo 104:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ntchito zanu ndi zochuluka, inu Yehova!+Zonsezo munazipanga mwanzeru zanu.+Dziko lapansi ladzaza ndi zinthu zimene munapanga.+
19 Zakumwamba zikulengeza ulemerero wa Mulungu.+Ndipo m’mlengalenga mukufotokoza ntchito ya manja ake.+
22 Tamandani Yehova inu ntchito zake zonse,+M’malo onse amene iye akulamulira.+Tamanda Yehova, iwe moyo wanga.+
24 Ntchito zanu ndi zochuluka, inu Yehova!+Zonsezo munazipanga mwanzeru zanu.+Dziko lapansi ladzaza ndi zinthu zimene munapanga.+