Salimo 104:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Zimalandira zimene mwazipatsa.+Mumatambasula dzanja lanu ndipo zimakhutira ndi zinthu zabwino.+