Genesis 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Motero, kumwamba ndi dziko lapansi ndi zonse za mmenemo zinamalizidwa kulengedwa.+ Yeremiya 32:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Inu mumasonyeza anthu masauzande ambiri kukoma mtima kosatha.+ Mumabwezera zolakwa za abambo kwa ana awo.*+ Inu ndinu Mulungu woona, wamkulu+ ndi wamphamvu,+ ndipo dzina lanu+ ndinu Yehova wa makamu.+ Yuda 14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ngakhalenso Inoki,+ wa m’badwo wa 7 kuchokera kwa Adamu, analosera za iwowa pamene anati: “Taonani! Yehova anabwera ndi miyandamiyanda ya oyera ake,*+
18 Inu mumasonyeza anthu masauzande ambiri kukoma mtima kosatha.+ Mumabwezera zolakwa za abambo kwa ana awo.*+ Inu ndinu Mulungu woona, wamkulu+ ndi wamphamvu,+ ndipo dzina lanu+ ndinu Yehova wa makamu.+
14 Ngakhalenso Inoki,+ wa m’badwo wa 7 kuchokera kwa Adamu, analosera za iwowa pamene anati: “Taonani! Yehova anabwera ndi miyandamiyanda ya oyera ake,*+