Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 12:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Kumalo amenewo, inuyo ndi mabanja anu muzidzadya zimenezi ndi kusangalala ndi zochita zanu zonse+ pamaso pa Yehova,+ chifukwa Yehova Mulungu wanu wakudalitsani.

  • 1 Samueli 12:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Chifukwa cha dzina lake lalikulu,+ Yehova sadzasiya+ anthu ake, pakuti Yehova wafuna kuti inuyo mukhale anthu ake.+

  • Salimo 100:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Dziwani kuti Yehova ndi Mulungu.+

      Iye ndi amene anatipanga, sitinadzipange tokha.+

      Ndife anthu ake ndi nkhosa zimene akuweta.+

  • Yesaya 54:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 “Pakuti Wokupanga Wamkulu+ ndiye mwamuna wako.+ Dzina lake ndi Yehova wa makamu,+ ndipo Woyera wa Isiraeli ndiye Wokuwombola.+ Iye adzatchedwa Mulungu wa dziko lonse lapansi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena