Salimo 63:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndikakumbukira inu ndili pabedi langa,+Pa nthawi za ulonda wa usiku* ndimasinkhasinkha za inu.+