Salimo 44:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Munapitikitsa anthu a mitundu ina ndi dzanja lanu,+Ndipo m’malo mwawo munakhazikitsa anthu anu.+Munagonjetsa mitundu ya anthu ndi kuipitikitsa.+
2 Munapitikitsa anthu a mitundu ina ndi dzanja lanu,+Ndipo m’malo mwawo munakhazikitsa anthu anu.+Munagonjetsa mitundu ya anthu ndi kuipitikitsa.+