1 Samueli 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mapazi a okhulupirika ake amawateteza.+Koma anthu oipa amawawononga mu mdima,+Pakuti munthu sakhala wapamwamba chifukwa cha mphamvu zake.+ Miyambo 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 mwa kuyang’anitsitsa njira zachiweruzo,+ ndipo adzateteza njira ya anthu ake okhulupirika.+
9 Mapazi a okhulupirika ake amawateteza.+Koma anthu oipa amawawononga mu mdima,+Pakuti munthu sakhala wapamwamba chifukwa cha mphamvu zake.+