Salimo 34:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Maso a Yehova ali pa olungama,+Ndipo makutu ake amamva kufuula kwawo kopempha thandizo.+ Salimo 55:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma ine ndidzafuulira Mulungu.+Ndipo Yehova adzandipulumutsa.+