Yobu 13:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pakuti inu mukupitiriza kundilembera zinthu zowawa,+Ndipo mukundipatsa zotsatira za zolakwa zimene ndinachita ndili mnyamata.+ Yeremiya 3:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Tagona pansi mwamanyazi+ ndipo manyazi athuwo akupitiriza kutiphimba.+ Zimenezi zakhala choncho chifukwa chakuti ifeyo ndi makolo athu, tachimwira Yehova Mulungu wathu+ ndipo sitinamvere mawu a Yehova Mulungu wathu+ kuyambira tili anyamata mpaka lero.”+
26 Pakuti inu mukupitiriza kundilembera zinthu zowawa,+Ndipo mukundipatsa zotsatira za zolakwa zimene ndinachita ndili mnyamata.+
25 Tagona pansi mwamanyazi+ ndipo manyazi athuwo akupitiriza kutiphimba.+ Zimenezi zakhala choncho chifukwa chakuti ifeyo ndi makolo athu, tachimwira Yehova Mulungu wathu+ ndipo sitinamvere mawu a Yehova Mulungu wathu+ kuyambira tili anyamata mpaka lero.”+