Salimo 65:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Inu Wakumva pemphero, anthu a mitundu yonse adzabwera kwa inu.+ 2 Akorinto 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Atamandike Mulungu ndi Atate+ wa Ambuye wathu Yesu Khristu, Tate wachifundo chachikulu+ ndi Mulungu amene amatitonthoza m’njira iliyonse,+
3 Atamandike Mulungu ndi Atate+ wa Ambuye wathu Yesu Khristu, Tate wachifundo chachikulu+ ndi Mulungu amene amatitonthoza m’njira iliyonse,+