Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 39:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Pamenepo mkaziyo anam’gwira malaya+ mnyamatayo n’kumuuza kuti: “Ugone nane basi!”+ Koma mnyamatayo anangovula malayawo n’kuwasiya m’manja mwa mkaziyo n’kuthawira panja.+

  • Miyambo 7:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 kuti utetezedwe kwa mkazi wachilendo,+ ndiponso kwa mkazi wochokera kwina amene amalankhula mawu okopa.+

  • Miyambo 22:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Pakamwa pa akazi achilendo pali ngati dzenje lakuya.+ Wotsutsidwa ndi Yehova adzagweramo.+

  • Miyambo 23:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Pakuti hule lili ngati dzenje lakuya,+ ndipo mkazi wachilendo ali ngati chitsime chopapatiza.

  • 1 Akorinto 6:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Kodi zoonadi inu simukudziwa kuti anthu osalungama sadzalowa mu ufumu wa Mulungu?+ Musasocheretsedwe. Adama,+ opembedza mafano,+ achigololo,+ amuna amene amagonedwa ndi amuna anzawo,+ amuna ogona amuna anzawo,+

  • 1 Akorinto 6:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Thawani dama.+ Tchimo lililonse limene munthu angachite ndi la kunja kwa thupi lake, koma amene amachita dama amachimwira thupi lake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena