Miyambo 12:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Palibe chopweteka chimene chidzagwere wolungama,+ koma anthu oipa ndi amene tsoka lizidzangowagwera.+ 2 Timoteyo 4:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ambuye adzandipulumutsa ku choipa chilichonse+ ndipo adzandisungira ufumu wake wakumwamba.+ Iye apatsidwe ulemerero mpaka muyaya. Ame.
21 Palibe chopweteka chimene chidzagwere wolungama,+ koma anthu oipa ndi amene tsoka lizidzangowagwera.+
18 Ambuye adzandipulumutsa ku choipa chilichonse+ ndipo adzandisungira ufumu wake wakumwamba.+ Iye apatsidwe ulemerero mpaka muyaya. Ame.