Miyambo 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kodi ugonabe mpaka liti, waulesiwe?+ Udzuka nthawi yanji kutulo tako?+ Miyambo 15:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Njira ya munthu waulesi ili ngati mpanda wa mitengo yaminga,+ koma njira ya anthu owongoka mtima imakhala yosalazidwa bwino.+
19 Njira ya munthu waulesi ili ngati mpanda wa mitengo yaminga,+ koma njira ya anthu owongoka mtima imakhala yosalazidwa bwino.+