Malaki 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Inu mwanena kuti, ‘Chifukwa chiyani?’+ Chifukwa chakuti Yehova wakudzudzulani popeza kuti aliyense wa inu wachitira zachinyengo mkazi amene anamukwatira ali mnyamata,+ ngakhale kuti iye anali mnzake komanso mkazi wa pangano lake.+
14 Inu mwanena kuti, ‘Chifukwa chiyani?’+ Chifukwa chakuti Yehova wakudzudzulani popeza kuti aliyense wa inu wachitira zachinyengo mkazi amene anamukwatira ali mnyamata,+ ngakhale kuti iye anali mnzake komanso mkazi wa pangano lake.+