Levitiko 19:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Usabere mnzako mwachinyengo+ ndipo usafwambe aliyense.+ Malipiro a munthu waganyu asagone m’nyumba mwako kufikira m’mawa.+
13 Usabere mnzako mwachinyengo+ ndipo usafwambe aliyense.+ Malipiro a munthu waganyu asagone m’nyumba mwako kufikira m’mawa.+