Miyambo 6:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Koma akapezeka, adzabweza zinthuzo kuwirikiza ka 7. Adzapereka zinthu zonse zamtengo wapatali za m’nyumba mwake.+ Mlaliki 11:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mnyamatawe, sangalala+ ndi unyamata wako, ndipo mtima wako ukusangalatse masiku a unyamata wako. Yenda m’njira za mtima wako ndiponso motsatira zimene maso ako akuona.+ Koma dziwa kuti Mulungu woona adzakuweruza chifukwa cha zonsezi.+ Maliro 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Wachititsa kuti mano anga aguluke ndi miyala.+ Wandipondaponda m’phulusa.+
31 Koma akapezeka, adzabweza zinthuzo kuwirikiza ka 7. Adzapereka zinthu zonse zamtengo wapatali za m’nyumba mwake.+
9 Mnyamatawe, sangalala+ ndi unyamata wako, ndipo mtima wako ukusangalatse masiku a unyamata wako. Yenda m’njira za mtima wako ndiponso motsatira zimene maso ako akuona.+ Koma dziwa kuti Mulungu woona adzakuweruza chifukwa cha zonsezi.+