1 Mafumu 21:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Yezebeli atangomva kuti Naboti waponyedwa miyala ndipo wafa, nthawi yomweyo anauza Ahabu kuti: “Nyamukani, katengeni munda wa mpesa wa Naboti Myezereeli+ umene anakana kukugulitsani uja, popeza Naboti salinso moyo koma wafa.” Miyambo 23:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Usasunthire kumbuyo malire akalekale,+ ndipo usalowe m’munda mwa ana amasiye.*+ Miyambo 28:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Munthu wochita zinthu mokhulupirika adzapeza madalitso ambiri,+ koma woyesetsa kuti apeze chuma mofulumira, sadzapitiriza kukhala wosalakwa.+
15 Yezebeli atangomva kuti Naboti waponyedwa miyala ndipo wafa, nthawi yomweyo anauza Ahabu kuti: “Nyamukani, katengeni munda wa mpesa wa Naboti Myezereeli+ umene anakana kukugulitsani uja, popeza Naboti salinso moyo koma wafa.”
20 Munthu wochita zinthu mokhulupirika adzapeza madalitso ambiri,+ koma woyesetsa kuti apeze chuma mofulumira, sadzapitiriza kukhala wosalakwa.+