Levitiko 27:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “‘Koma ngati chopereka chake ndi nyama yonga imene anthu amapereka nsembe kwa Yehova, iliyonseyo imene angapereke kwa Yehova izikhala yopatulika.+
9 “‘Koma ngati chopereka chake ndi nyama yonga imene anthu amapereka nsembe kwa Yehova, iliyonseyo imene angapereke kwa Yehova izikhala yopatulika.+