Salimo 119:71 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 71 Zili bwino kuti ndasautsika,+Kuti ndiphunzire malamulo anu.+ Miyambo 22:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Uchitsiru umakhazikika mumtima mwa mwana.+ Koma ndodo yomulangira* ndi imene imauthamangitsira kutali ndi iye.+
15 Uchitsiru umakhazikika mumtima mwa mwana.+ Koma ndodo yomulangira* ndi imene imauthamangitsira kutali ndi iye.+