Salimo 21:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mfumuyo inakupemphani moyo. Ndipo munaipatsadi,+Munaipatsa masiku ochuluka kuti ikhale mpaka kalekale, ndithu mpaka muyaya.+ Miyambo 10:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kuopa Yehova kudzawonjezera masiku,+ koma zaka za anthu oipa zidzafupikitsidwa.+
4 Mfumuyo inakupemphani moyo. Ndipo munaipatsadi,+Munaipatsa masiku ochuluka kuti ikhale mpaka kalekale, ndithu mpaka muyaya.+