2 Samueli 15:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Iwe wabwera dzulo lomweli, kodi lero uyende+ ndi ife kupita kulikonse kumene ine ndikupita? Bwerera, tenga abale ako ndi kubwerera nawo limodzi, ndipo Yehova akusonyeze kukoma mtima kosatha+ ndi kukhulupirika kwake!”+ Hoseya 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Koma iwe ubwerere kwa Mulungu wako.+ Usonyeze kukoma mtima kosatha+ ndi chilungamo+ ndipo nthawi zonse uziyembekezera Mulungu wako.+
20 Iwe wabwera dzulo lomweli, kodi lero uyende+ ndi ife kupita kulikonse kumene ine ndikupita? Bwerera, tenga abale ako ndi kubwerera nawo limodzi, ndipo Yehova akusonyeze kukoma mtima kosatha+ ndi kukhulupirika kwake!”+
6 “Koma iwe ubwerere kwa Mulungu wako.+ Usonyeze kukoma mtima kosatha+ ndi chilungamo+ ndipo nthawi zonse uziyembekezera Mulungu wako.+