Miyambo 13:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Munthu woyenda ndi anthu anzeru adzakhala wanzeru,+ koma wochita zinthu ndi anthu opusa adzapeza mavuto.+ 1 Akorinto 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chimene mukudzitamira+ si chabwino ayi. Kodi simukudziwa kuti chofufumitsa chaching’ono chimafufumitsa+ mtanda wonse?+
20 Munthu woyenda ndi anthu anzeru adzakhala wanzeru,+ koma wochita zinthu ndi anthu opusa adzapeza mavuto.+
6 Chimene mukudzitamira+ si chabwino ayi. Kodi simukudziwa kuti chofufumitsa chaching’ono chimafufumitsa+ mtanda wonse?+